Ekisodo 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ansembe ochita zamatsenga aja sanathe kuonekera pamaso pa Mose chifukwa cha zithupsazo, popeza zinatuluka pa ansembewo ndi pa Aiguputo onse.+
11 Ansembe ochita zamatsenga aja sanathe kuonekera pamaso pa Mose chifukwa cha zithupsazo, popeza zinatuluka pa ansembewo ndi pa Aiguputo onse.+