-
Ekisodo 9:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Pofika pano ndikanakhala nditatambasula kale dzanja langa nʼkupha iweyo komanso anthu ako ndi mliri woopsa, ndipo ndikanakufafanizani padziko lapansi.
-