Ekisodo 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsopano Yehova anauza Mose kuti: “Tambasula dzanja lako nʼkuloza kumwamba kuti matalala agwe mʼdziko lonse la Iguputo,+ kuti agwere anthu, nyama ndi zomera zonse mʼdziko la Iguputo.”+
22 Tsopano Yehova anauza Mose kuti: “Tambasula dzanja lako nʼkuloza kumwamba kuti matalala agwe mʼdziko lonse la Iguputo,+ kuti agwere anthu, nyama ndi zomera zonse mʼdziko la Iguputo.”+