-
Ekisodo 9:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Kenako Farao anatumiza atumiki ake kukaitana Mose ndi Aroni nʼkuwauza kuti: “Tsopano ndachimwa. Yehova ndi wolungama, koma ine ndi anthu anga ndife olakwa.
-