Ekisodo 9:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Choncho Mose anamuyankha kuti: “Ndikangotuluka mumzinda uno, ndikweza manja anga kwa Yehova. Mabingu asiya ndipo matalala sapitirizanso kugwa kuti mudziwe kuti dziko lapansi ndi la Yehova.+
29 Choncho Mose anamuyankha kuti: “Ndikangotuluka mumzinda uno, ndikweza manja anga kwa Yehova. Mabingu asiya ndipo matalala sapitirizanso kugwa kuti mudziwe kuti dziko lapansi ndi la Yehova.+