Ekisodo 9:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndiyeno Mose anachoka pamaso pa Farao nʼkutuluka mumzindawo. Kenako anakweza manja ake kwa Yehova, ndipo mabingu ndi matalala zinasiya, mvulanso inasiya kugwa padziko lapansi.+
33 Ndiyeno Mose anachoka pamaso pa Farao nʼkutuluka mumzindawo. Kenako anakweza manja ake kwa Yehova, ndipo mabingu ndi matalala zinasiya, mvulanso inasiya kugwa padziko lapansi.+