Ekisodo 9:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Choncho Farao anapitiriza kuumitsa mtima wake ndipo sanalole kuti Aisiraeli apite, mogwirizana ndi zimene Yehova ananena kudzera mwa Mose.+
35 Choncho Farao anapitiriza kuumitsa mtima wake ndipo sanalole kuti Aisiraeli apite, mogwirizana ndi zimene Yehova ananena kudzera mwa Mose.+