Ekisodo 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Pita kwa Farao chifukwa ndalola kuti iye ndi atumiki ake aumitse mitima yawo,+ kuti ndichite zizindikiro zanga pamaso pake.+
10 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Pita kwa Farao chifukwa ndalola kuti iye ndi atumiki ake aumitse mitima yawo,+ kuti ndichite zizindikiro zanga pamaso pake.+