Ekisodo 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndachita zimenezi kuti mufotokozere ana anu ndi zidzukulu zanu mmene ndakhaulitsira Iguputo komanso zizindikiro zimene ndachitira Aiguputo.+ Ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.”
2 Ndachita zimenezi kuti mufotokozere ana anu ndi zidzukulu zanu mmene ndakhaulitsira Iguputo komanso zizindikiro zimene ndachitira Aiguputo.+ Ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.”