Ekisodo 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho Mose ndi Aroni anapita kwa Farao nʼkukamuuza kuti: “Yehova Mulungu wa Aheberi wanena kuti, ‘Kodi upitiriza kukana kundigonjera mpaka liti?+ Lola anthu anga kuti apite kukanditumikira.
3 Choncho Mose ndi Aroni anapita kwa Farao nʼkukamuuza kuti: “Yehova Mulungu wa Aheberi wanena kuti, ‘Kodi upitiriza kukana kundigonjera mpaka liti?+ Lola anthu anga kuti apite kukanditumikira.