Ekisodo 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Dzombelo lidzakuta nthaka yonse ndipo simudzatha kuona dothi. Lidzadya chilichonse chotsalira komanso chilichonse chimene matalala sanawononge. Ndipo lidzadya mitengo yanu yonse imene yayamba kumera.+
5 Dzombelo lidzakuta nthaka yonse ndipo simudzatha kuona dothi. Lidzadya chilichonse chotsalira komanso chilichonse chimene matalala sanawononge. Ndipo lidzadya mitengo yanu yonse imene yayamba kumera.+