Ekisodo 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Dzombelo lidzadzaza mʼnyumba zanu, mʼnyumba zonse za atumiki anu ndi mʼnyumba za mu Iguputo monse. Lidzadzaza mʼnyumbazi mpaka kufika poti makolo anu ndi makolo a makolo anu sanaonepo chibadwire chawo.’”+ Atatero, Mose anachoka pamaso pa Farao.
6 Dzombelo lidzadzaza mʼnyumba zanu, mʼnyumba zonse za atumiki anu ndi mʼnyumba za mu Iguputo monse. Lidzadzaza mʼnyumbazi mpaka kufika poti makolo anu ndi makolo a makolo anu sanaonepo chibadwire chawo.’”+ Atatero, Mose anachoka pamaso pa Farao.