Ekisodo 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno Mose anati: “Tipita ndi achinyamata athu, achikulire athu, ana athu aamuna ndi ana athu aakazi pamodzi ndi nkhosa ndi ngʼombe zathu,+ chifukwa tikukachitira Yehova chikondwerero.”+
9 Ndiyeno Mose anati: “Tipita ndi achinyamata athu, achikulire athu, ana athu aamuna ndi ana athu aakazi pamodzi ndi nkhosa ndi ngʼombe zathu,+ chifukwa tikukachitira Yehova chikondwerero.”+