Ekisodo 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Farao anawauza kuti: “Ngati ndingalole kuti inu pamodzi ndi ana anu mupite, ndiye kuti Yehova alidi ndi inu.+ Ndikudziwa kuti mukufuna kuchita chinachake choipa.
10 Farao anawauza kuti: “Ngati ndingalole kuti inu pamodzi ndi ana anu mupite, ndiye kuti Yehova alidi ndi inu.+ Ndikudziwa kuti mukufuna kuchita chinachake choipa.