-
Ekisodo 10:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Tambasula dzanja lako nʼkuloza dziko la Iguputo kuti dzombe ligwe mʼdziko lonselo nʼkudya zomera zonse zamʼdzikomo, chilichonse chimene matalala sanawononge.”
-