-
Ekisodo 10:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Zitatero Mose analoza dziko lonse la Iguputo ndi ndodo yake, ndipo Yehova anachititsa mphepo yochokera kumʼmawa kuwomba padziko lonselo, masana onse ndi usiku onse. Mʼmawa kutacha mphepoyo inabweretsa dzombe.
-