Ekisodo 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Dzombelo linafika mʼdziko lonse la Iguputo nʼkufalikira mʼmadera onse adzikolo+ ndipo linawononga kwambiri.+ Dzombe lambiri ngati limeneli linali lisanagwepo nʼkale lonse ndipo silidzagwanso lambiri ngati limeneli.
14 Dzombelo linafika mʼdziko lonse la Iguputo nʼkufalikira mʼmadera onse adzikolo+ ndipo linawononga kwambiri.+ Dzombe lambiri ngati limeneli linali lisanagwepo nʼkale lonse ndipo silidzagwanso lambiri ngati limeneli.