-
Ekisodo 10:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Dzombelo linakuta nthaka yonse yamʼdzikolo ndipo dziko linachita mdima. Dzombelo linadya zomera zonse zamʼdzikolo ndi zipatso zonse zamʼmitengo zimene sizinawonongeke ndi matalala, moti sipanatsale chobiriwira chilichonse mʼmitengo kapena mʼminda mʼdziko lonse la Iguputo.
-