Ekisodo 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Komabe Yehova analola Farao kuumitsa mtima wake+ moti sanalole kuti Aisiraeli achoke.