Ekisodo 10:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Zitatero Farao anaitana Mose nʼkumuuza kuti: “Pitani, katumikireni Yehova.+ Koma nkhosa zanu ndi ngʼombe zanu simupita nazo. Ana anunso mungathe kupita nawo.”
24 Zitatero Farao anaitana Mose nʼkumuuza kuti: “Pitani, katumikireni Yehova.+ Koma nkhosa zanu ndi ngʼombe zanu simupita nazo. Ana anunso mungathe kupita nawo.”