Ekisodo 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma Mose anati: “Inuyo mutipatse* nyama zokapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zina, kuti tikazipereke kwa Yehova Mulungu wathu.+
25 Koma Mose anati: “Inuyo mutipatse* nyama zokapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zina, kuti tikazipereke kwa Yehova Mulungu wathu.+