26 Ziweto zathu tipitanso nazo. Sitidzasiya chiweto ngakhale chimodzi, chifukwa tikagwiritsa ntchito zina mwa ziweto zimenezi polambira Yehova Mulungu wathu. Koma panopa sitikudziwa kuti tikapereka chiyani polambira Yehova mpaka titakafika kumeneko.”