Ekisodo 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Choncho Yehova analola Farao kuumitsa mtima wake ndipo sanalole kuti Aisiraeli achoke.+