Ekisodo 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano uza anthu kuti mwamuna aliyense ndi mkazi aliyense apemphe kwa munthu wokhala naye pafupi zinthu zasiliva ndi zagolide.”+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:2 Nsanja ya Olonda,3/15/2004, tsa. 26
2 Tsopano uza anthu kuti mwamuna aliyense ndi mkazi aliyense apemphe kwa munthu wokhala naye pafupi zinthu zasiliva ndi zagolide.”+