Ekisodo 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ngakhale galu sadzauwa aliyense wa Aisiraeli, sadzauwa anthu kapena ziweto zawo, kuti mudziwe kuti Yehova akhoza kuchitira Aisiraeli zinthu zosiyana ndi zimene angachitire Aiguputo.’+
7 Ngakhale galu sadzauwa aliyense wa Aisiraeli, sadzauwa anthu kapena ziweto zawo, kuti mudziwe kuti Yehova akhoza kuchitira Aisiraeli zinthu zosiyana ndi zimene angachitire Aiguputo.’+