Ekisodo 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo atumiki anu onsewa adzabwera kwa ine nʼkundigwadira komanso kundiweramira. Iwo adzanena kuti, ‘Pita, iweyo ndi anthu onse amene amakutsatira.’+ Akadzatero ndidzapitadi.” Atanena mawu amenewa anachoka kwa Farao atakwiya.
8 Ndipo atumiki anu onsewa adzabwera kwa ine nʼkundigwadira komanso kundiweramira. Iwo adzanena kuti, ‘Pita, iweyo ndi anthu onse amene amakutsatira.’+ Akadzatero ndidzapitadi.” Atanena mawu amenewa anachoka kwa Farao atakwiya.