Ekisodo 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mose ndi Aroni anachita zodabwitsa zonsezi pamaso pa Farao.+ Koma Yehova analola Farao kuumitsa mtima wake, moti sanalole kuti Aisiraeli achoke mʼdziko lake.+
10 Mose ndi Aroni anachita zodabwitsa zonsezi pamaso pa Farao.+ Koma Yehova analola Farao kuumitsa mtima wake, moti sanalole kuti Aisiraeli achoke mʼdziko lake.+