Ekisodo 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Uzani gulu lonse la Isiraeli kuti, ‘Pa tsiku la 10 la mwezi uno mabanja onse ochokera mwa kholo limodzi adzatenge nkhosa imodziimodzi,+ banja lililonse lidzatenge nkhosa imodzi.
3 Uzani gulu lonse la Isiraeli kuti, ‘Pa tsiku la 10 la mwezi uno mabanja onse ochokera mwa kholo limodzi adzatenge nkhosa imodziimodzi,+ banja lililonse lidzatenge nkhosa imodzi.