Ekisodo 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nkhosa yanuyo ikhale yopanda chilema,+ yamphongo, yachaka chimodzi. Mungatenge mwana wa nkhosa kapena wa mbuzi.
5 Nkhosa yanuyo ikhale yopanda chilema,+ yamphongo, yachaka chimodzi. Mungatenge mwana wa nkhosa kapena wa mbuzi.