Ekisodo 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Adzatenge magazi nʼkuwawaza pamafelemu awiri amʼmbali mwa khomo ndi pafelemu lapamwamba pa chitseko. Adzachite zimenezi panyumba zimene adzadyeremo nkhosayo.+
7 Adzatenge magazi nʼkuwawaza pamafelemu awiri amʼmbali mwa khomo ndi pafelemu lapamwamba pa chitseko. Adzachite zimenezi panyumba zimene adzadyeremo nkhosayo.+