-
Ekisodo 12:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Musadzaidye yaiwisi, yowiritsa kapena yophika ndi madzi, koma mudzadye yowotcha pamoto. Mudzawotche mutu wake pamodzi ndi ziboda ndiponso zamʼmimba.
-