Ekisodo 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Magaziwo adzakhala chizindikiro panyumba zimene mudzakhalemo. Ndipo ine ndidzaona magaziwo nʼkukupitirirani, moti mliriwo sudzakugwerani nʼkukuwonongani ndikamadzalanga dziko la Iguputo.+
13 Magaziwo adzakhala chizindikiro panyumba zimene mudzakhalemo. Ndipo ine ndidzaona magaziwo nʼkukupitirirani, moti mliriwo sudzakugwerani nʼkukuwonongani ndikamadzalanga dziko la Iguputo.+