19 Kwa masiku 7 mʼnyumba zanu musamadzapezeke ufa wokanda wokhala ndi zofufumitsa, chifukwa aliyense amene wadya chakudya chokhala ndi zofufumitsa, kaya ndi mlendo kapena mbadwa ya Isiraeli,+ munthu ameneyo adzaphedwa kuti asakhalenso pagulu la Isiraeli.+