Ekisodo 12:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mwamsanga, Mose anaitana akulu onse a Isiraeli+ nʼkuwauza kuti: “Pitani mukasankhire mabanja anu onse ana a ziweto* nʼkuwapha kuti ikhale nsembe ya Pasika.
21 Mwamsanga, Mose anaitana akulu onse a Isiraeli+ nʼkuwauza kuti: “Pitani mukasankhire mabanja anu onse ana a ziweto* nʼkuwapha kuti ikhale nsembe ya Pasika.