Ekisodo 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mukatero mukatenge kamtengo ka hisope* nʼkukaviika mʼbeseni la magazi nʼkuwawaza pafelemu lapamwamba pa chitseko, ndipo ena mwa magaziwo muwawaze pamafelemu awiri amʼmbali mwa khomo. Aliyense asadzatuluke mʼnyumba yake mpaka mʼmawa.
22 Mukatero mukatenge kamtengo ka hisope* nʼkukaviika mʼbeseni la magazi nʼkuwawaza pafelemu lapamwamba pa chitseko, ndipo ena mwa magaziwo muwawaze pamafelemu awiri amʼmbali mwa khomo. Aliyense asadzatuluke mʼnyumba yake mpaka mʼmawa.