Ekisodo 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno Yehova akamadzapita kukapha Aiguputo ndi mliri, nʼkuona magazi pamafelemu apamwamba pa zitseko zanu ndi mafelemu awiri amʼmbali mwa khomo, Yehova adzapitirira khomo limenelo ndipo sadzalola mliri wa imfa kulowa mʼnyumba zanu.+
23 Ndiyeno Yehova akamadzapita kukapha Aiguputo ndi mliri, nʼkuona magazi pamafelemu apamwamba pa zitseko zanu ndi mafelemu awiri amʼmbali mwa khomo, Yehova adzapitirira khomo limenelo ndipo sadzalola mliri wa imfa kulowa mʼnyumba zanu.+