Ekisodo 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Choncho muzichita chikondwerero chimenechi. Limeneli ndi lamulo kwa inu ndi kwa ana anu mpaka kalekale.+
24 Choncho muzichita chikondwerero chimenechi. Limeneli ndi lamulo kwa inu ndi kwa ana anu mpaka kalekale.+