Ekisodo 12:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiyeno ana anu akadzakufunsani kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani timachita mwambo umenewu?’+