Ekisodo 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho Aisiraeli anachoka nʼkukachita mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose ndi Aroni.+ Anachitadi zomwezo. Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:28 Nsanja ya Olonda,12/15/1995, tsa. 12
28 Choncho Aisiraeli anachoka nʼkukachita mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose ndi Aroni.+ Anachitadi zomwezo.