Ekisodo 12:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Zitatero Farao, atumiki ake onse ndi Aiguputo onse anadzuka usiku umenewo. Ndipo anthu anayamba kulira kwambiri mʼdziko lonse la Iguputo, chifukwa panalibe banja ngakhale limodzi limene linalibe maliro.+
30 Zitatero Farao, atumiki ake onse ndi Aiguputo onse anadzuka usiku umenewo. Ndipo anthu anayamba kulira kwambiri mʼdziko lonse la Iguputo, chifukwa panalibe banja ngakhale limodzi limene linalibe maliro.+