Ekisodo 12:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mutengenso nkhosa ndi ngʼombe zanu monga mwanenera ndipo muzipita.+ Komanso mukandipemphere kwa Mulungu kuti andidalitse.”
32 Mutengenso nkhosa ndi ngʼombe zanu monga mwanenera ndipo muzipita.+ Komanso mukandipemphere kwa Mulungu kuti andidalitse.”