Ekisodo 12:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Choncho Yehova anachititsa kuti Aiguputo akomere mtima anthu ake, moti Aiguputowo anawapatsa zinthu zonse zimene anapempha ndipo iwo anatenga zinthu zambiri za Aiguputo.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:36 Nsanja ya Olonda,3/15/2004, tsa. 2611/1/1999, tsa. 3012/1/1994, tsa. 13
36 Choncho Yehova anachititsa kuti Aiguputo akomere mtima anthu ake, moti Aiguputowo anawapatsa zinthu zonse zimene anapempha ndipo iwo anatenga zinthu zambiri za Aiguputo.+