Ekisodo 12:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Umenewu ndi usiku umene azidzakondwerera kuti Yehova anawatulutsa mʼdziko la Iguputo. Yehova anafuna kuti Aisiraeli onse, azidzachita chikondwerero chimenechi mʼmibadwo yawo yonse pokumbukira usiku umenewu.+
42 Umenewu ndi usiku umene azidzakondwerera kuti Yehova anawatulutsa mʼdziko la Iguputo. Yehova anafuna kuti Aisiraeli onse, azidzachita chikondwerero chimenechi mʼmibadwo yawo yonse pokumbukira usiku umenewu.+