Ekisodo 12:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Muzidyera mʼnyumba imodzi. Musatuluke panja ndi nyama iliyonse komanso musaphwanye fupa lililonse la nyamayo.+
46 Muzidyera mʼnyumba imodzi. Musatuluke panja ndi nyama iliyonse komanso musaphwanye fupa lililonse la nyamayo.+