Ekisodo 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Mose anauza anthuwo kuti: “Muzikumbukira tsiku lalero limene mwatuluka mu Iguputo,+ mʼnyumba ya ukapolo, chifukwa Yehova wakutulutsani mʼdzikoli ndi dzanja lake lamphamvu.+ Choncho musadye chilichonse chokhala ndi zofufumitsa.
3 Kenako Mose anauza anthuwo kuti: “Muzikumbukira tsiku lalero limene mwatuluka mu Iguputo,+ mʼnyumba ya ukapolo, chifukwa Yehova wakutulutsani mʼdzikoli ndi dzanja lake lamphamvu.+ Choncho musadye chilichonse chokhala ndi zofufumitsa.