Ekisodo 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova akadzakulowetsani mʼdziko la Akanani, Ahiti, Aamori, Ahivi ndi Ayebusi,+ dziko loyenda mkaka ndi uchi,+ limene analumbira kwa makolo anu kuti adzakupatsani,+ muzidzachita mwambo umenewu mʼmwezi uno.
5 Yehova akadzakulowetsani mʼdziko la Akanani, Ahiti, Aamori, Ahivi ndi Ayebusi,+ dziko loyenda mkaka ndi uchi,+ limene analumbira kwa makolo anu kuti adzakupatsani,+ muzidzachita mwambo umenewu mʼmwezi uno.