-
Ekisodo 13:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Farao atalola kuti Aisiraeli apite, Mulungu sanawadutsitse mʼdziko la Afilisiti ngakhale kuti inali njira yaifupi, chifukwa Mulungu anati: “Anthu angasinthe maganizo akakumana ndi nkhondo ndipo angabwerere ku Iguputo.”
-