Ekisodo 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mose anatenganso mafupa a Yosefe chifukwa Yosefe analumbiritsa ana a Isiraeli kuti: “Ndithudi, Mulungu adzakukumbukirani, ndipo pochoka kuno mudzatenge mafupa anga.”+
19 Mose anatenganso mafupa a Yosefe chifukwa Yosefe analumbiritsa ana a Isiraeli kuti: “Ndithudi, Mulungu adzakukumbukirani, ndipo pochoka kuno mudzatenge mafupa anga.”+