Ekisodo 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza Aisiraeli kuti abwerere nʼkumanga msasa pafupi ndi Pihahiroti, pakati pa Migidoli ndi nyanja, koma moyangʼanizana ndi Baala-zefoni.+ Mumange msasa wanu pafupi ndi nyanja, patsogolo pa Baala-zefoni.
2 “Uza Aisiraeli kuti abwerere nʼkumanga msasa pafupi ndi Pihahiroti, pakati pa Migidoli ndi nyanja, koma moyangʼanizana ndi Baala-zefoni.+ Mumange msasa wanu pafupi ndi nyanja, patsogolo pa Baala-zefoni.