5 Kenako mfumu ya Iguputo inauzidwa kuti Aisiraeli athawa. Nthawi yomweyo mtima wa Farao ndi atumiki ake unasinthanso ataganizira za Aisiraeli,+ moti anati: “Nʼchifukwa chiyani tachita zimenezi? Nʼchifukwa chiyani talola kuti akapolo athu Aisiraeli achoke?”